Nzeru Za Akuluakulu (Wisdom of the Elders)

Опубликовано: 01 Июль 2026
на канале: Fletcher Matandika
200
like

Kalongosoledwe:
Nyimbo iyi ikukamba za mwambi wakuti, "Chimene munthu wamkulu amaona atakhala pansi, mwana sangaone atayimirira." Nyimboyi ikulimbikitsa achinyamata kuti azimvera nzeru za makolo, ndipo kuti nzeru za makolo awo ndi mphatso ya Mulungu.

Nyimbo ndi yopangidwa ndi Suno AI; kanema ndi wopangidwa ndi Revid AI.